Yankhani Mafunso okhudza Korona!

Dziyeseni zomwe mukudziwa pankhani za korona poyankha mafunsowa.

Which of the following are symptoms of coronavirus?

Sankhani zonse zomwe zili zoyenera

Ndi chiti mwa zotsatirazi chomwe chili chizindikiro cha koronavayilasi?

Sankhani zonse zomwe zili zoyenera

Which of the following is TRUE about Coronavirus?

Sankhani zonse zomwe zili zoyenera

Ndi chiganizo chiti mwa ziganizo zotsatirazi chomwe chikukamba ZOONA za Koronavayilasi?

Sankhani zonse zomwe zili zoyenera

Pitani pa tsamba loyamba