Chiyambireni COVID-19, munkalephera kupeza chakudya chomwe mumafuna chifukwa panalibe ndalama zokwanira?
Sankhani limodzi
Since COVID-19, were you not able to get the food you wanted because there wasn’t enough money?
Since COVID-19, did you skip a meal because your family didn’t have enough food?
Chiyambireni COVID-19, munadumphitsako kudya patsiku chifukwa chakuti m’banja mwanu munali chakudya chosakwanira?
Since COVID-19, has the size of your meal been cut because your family didn’t have enough food?
Chiyambireni COVID-19, munachepetsako mlingo wa chakudya chomwe mumadya chifukwa m’banja mwanu munali chakudya chosakwanira?
Since COVID-19, were you hungry but didn’t eat because your family didn’t have enough food?
Chiyambireni COVID-19, munakhalako ndi njala koma osadya chifukwa chakuti m’banja mwanu munali chakudya chosakwanira?
Chiyambireni COVID-19, pali nthawi yomwe munamvako kutopa kapena kufooka chifukwa m’banja mwanu munali chakudya chosakwanira?
Since COVID-19, did you feel tired or weak because your family didn’t have enough food to eat?
Since COVID-19, how much have you eaten fast foods or street foods?
Chiyambireni COVID-19, mwadya mochuluka bwanji zakudya zogulitsidwa zophikaphika kumsika kapena m’mbali mwamseu?
Chiyambireni COVID-19, mwadya mochuluka bwanji zakudya zophikidwa ku fakitale zomwe zimaikidwa mu paketi, katoni kapena chitini?
Zakudya zakufakitale zomwe zimaikidwa mu paketi, katoni kapena chitini zimaikidwa zinthu zochititsa kuti zikhale nthawi yaitali zisanaonongeke. Kawirikawiri, zakudyazi zimapangidwa posakaniza zinthu zingapo zopangira kapena kuphikira zakudya.
Since COVID-19, how much have you eaten processed foods?
Processed foods are food items that had a series of operations performed to change or preserve them. Processed foods are those that typically come in a box or bag and contain more than one item on the list of ingredients.
Chakudya mumadyela kuti
© The Internet of Good Things