Kafukufuku

Survey Graphic.png

Moni!

A IoGT ali ndi mafuso omwe akufuna akufu akufunseni okhudzana ndi mene mukuionela webusaiti ino. Mayankho anu ndi ofunika kwa ife. Tiyankheni mafunso ali musimu. imutenga nthawi yopirila mphindi imodzi.

Mayankho anu akhala achinsinsi ndipo adzagwiritsidwa ntchito ndi akufukufuku omwe akugwira ntchito yoonetsetsa kuti IoGT ikupezeka mosavuta ndipo ikugwira ntchito mosavutaso.

Zikomo kwambiri!

Kodi ndinu akazi kapena amuna?

Sankhani limodzi

Kodi muli ndi zaka zingati?

Ndimakhala ku...

Sankhani limodzi

Kodi mumapanga chani m'moyo wanu?

Sankhani limodzi

Kodi tsamba la IoGT munalowapo kangati m'chaka chapitachi?

Sankhani limodzi

IoGT ndimaigwiritsa ntchito pafupi pafupi ku..…

Sankhani limodzi

Kodi zomwe zimakukanikitsani kugwiritsa ntchito IoGT ndiziti?

Sankhani zonse zomwe zili zoyenera

Ndimasangala kugwiritsa ntchito IoGT.

Sankhani limodzi

Kupeza zomwe ndikufuna pa IoGT nkosavuta.

Sankhani limodzi

Zomwe zili pa IoGT nzofunika.

Sankhani limodzi

Which topics on IoGT do you find useful?

Sankhani zonse zomwe zili zoyenera

Zilipo zina zomwe mungafune mutazipeza pa tsamba la IoGT lino?

Losankha

Zina zomwe mungafune muzipanga pa IoGT pano ndi monga ziti?

Sankhani zonse zomwe zili zoyenera

Pitani pa tsamba loyamba