Kafukufuku Wachinsinsi wa Umoyo ogonana ndi HIV pa nthawi ya COVID

Tikufuna kudziwa za mmene mliri wa COVID wakhudzila umoyo ogonona, uchembere wabwino ndi HIV.

Ndinu mwamuna kapena mkazi?

Sankhani limodzi

What is your age?

Sankhani limodzi

What is your gender?

Sankhani limodzi

Muli ndi zaka zingati?

Sankhani limodzi

Fotokozani komwe mumakhala.

Sankhani limodzi

Describe where you live?

Sankhani limodzi

Since the onset of the COVID-19 epidemic, do you believe that in your community...

Sankhani limodzi

Chiyambireni mlili wa COVID-19, kodi mukukhulupirira kuti m’dera lanu...

Sankhani limodzi

During COVID-19, were you able to access sexual and reproductive health and HIV services like testing, ARTs, and contraception, if you needed them?

Sankhani limodzi

Kodi panyengo ya COVID-19, mumakwanitsa kupeza chithandizo chokhudza umoyo wogonana ndi uchembere wabwino komanso chokhudza HIV, monga kuyezetsa magazi, kulandira mankhwala oonjezera chitetezo m’nthupi, komanso njira zakulera, panthawi imene zimafunikila?

Sankhani limodzi

When you accessed any SRH or HIV service, was the health staff friendly to you?

Sankhani limodzi

Pokapeza chithandizo chokhudza umoyo wogonana ndi uchembere wabwino, kapena chokhudza kachilombo ka HIV, ogwira ntchito kuchipatala ankakuthandizani mwachikondi?

Sankhani limodzi

The main barrier for me to see a health care provider when I needed a service like HIV testing, ARTs, contraception, pregnancy tests or services or treatment for a sexually transmitted infection (STI) is:

Sankhani limodzi

Vuto lalikulu lomwe ndinkakumana nalo pofuna chithandizo kuchipatala monga kuyezetsa magazi, kulandira mankhwala oonjezera chitetezo, njira zakulera, kuyezetsa pathupi, kapenanso chithandizo cha matenda opatsirana pogonana ndi:

Sankhani limodzi

If you urgently needed a sexual and reproductive health service during COVID 19, which of the following services have you accessed?

Losankha
Sankhani zonse zomwe zili zoyenera

Mu nyengo ya COVID-19, mwakhala mukukwanitsa kupeza makondomu panthawi imene amafunikira?

Sankhani limodzi

How did you access the services you needed?

Sankhani limodzi

Vuto lalikulu lomwe ndinkakumana nalo ndikafuna kupeza makondomu panthawi yomwe akufunikira linali:

Sankhani limodzi

During COVID-19, have you been able to access condoms if you needed them?

Sankhani limodzi

Kodi mukudziwako munthu wina wake amene ali ndi kachilombo ka HIV ndipo amavutika kupeza chithandizo cha mankwala oonjezera chitetezo m’nthupi (ma ARV) panyengo ya COVID-19?

Sankhani limodzi

The main barrier for me to get timely access to condoms if I needed them was:

Sankhani limodzi

Kodi mukukhulupirira kuti muli pachiopsezo chotenga matenda a COVID-19?

Sankhani limodzi

Ndikufuna kupeza mauthenga okhudza umoyo wogonana ndi uchembere wabwino komanso/kapena HIV kudzera

Sankhani mayankho onse oyenera

Do you know of anyone who is HIV positive who has found it difficult to access treatment (ARVs) during COVID?

Sankhani limodzi

Do you believe you are at risk of contracting COVID-19?

Sankhani limodzi

Mukafuna chithandizo chachangu chokhudza umoyo wogonana ndi uchembere wabwino panyengo ya mlili wa COVID-19, ndi ziti mwa zinthu zotsatirazi zimene munakwanitsa kupeza?

Losankha
Chongani zonse zimene munakwanitsa kupeza

I would like to access information on sexual reproductive health and/or HIV at this time through

Sankhani zonse zomwe zili zoyenera

Chithandizo chomwe chinkafunikira munkachipeza motani?

Sankhani limodzi

Pitani pa tsamba loyamba