Kodi ndinu akazi kapena amuna?
Akazi
Amuna
Zina
Kumudzi
Pa Boma
Kufupi kwambiri ndi tawuni.
Mu mzinda waukulu
Kodi mumapanga chani m'moyo wanu?
Sindigwira ntchito (sindili pa ntchito/sindili pa sukulu)
Sindigwira ntchito (Ndili pa sukulu)
Ndimapanga zanga.
Ndimagwira ganyu.
Ndimagwira ntchito yokhazikika.
Kodi tsamba la IoGT munalowapo kangati m'chaka chapitachi?
Kopitirira ka modzi pa sabata
Kamodzi pa sabata
Kamodzi pa mwezi
Mwa apo ndi apo
Kamodzi
IoGT ndimaigwiritsa ntchito pafupi pafupi ku..…
Ku nyumba
Ku sukulu
Ku ntchito
Ndikakhala koyenda
Kodi zomwe zimakukanikitsani kugwiritsa ntchito IoGT ndiziti?
Ndimasangala kugwiritsa ntchito IoGT.
1 (Ata! mpang'ono pomwe)
2 (Ata!)
3 (Ndili pakatii kati. Imandisangalatsa komanso sindisangalatsa)
4 (Imandisangalatsa)
5 (Imandisangalata kwambiri)
Kupeza zomwe ndikufuna pa IoGT nkosavuta.
1 (ndikovuta kwambiri)
2 (ndikovuta)
3 (Ndipakati kati. Nkovuta koma pena nkosavuta)
4 (Nkosavuta kwambiri)
5 (Nkosavuta)
Zomwe zili pa IoGT nzofunika.
1 (nzofunika kwambiri)
2 (nzofunika)
3 (zili pakati kati- zofunika komanso zosafunika)
4 (nzosafunika)
5 (nzosafunika konse)
Which topics on IoGT do you find useful?
Zina zomwe mungafune muzipanga pa IoGT pano ndi monga ziti?